2 Mafumu 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi, anakonzera Yehoramu chiwembu. Yehoramu ankalondera Ramoti-giliyadi+ pamodzi ndi Aisiraeli onse, chifukwa cha Hazaeli+ mfumu ya Siriya. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:14 Nsanja ya Olonda,11/15/2011, tsa. 3
14 Ndiyeno Yehu+ mwana wa Yehosafati mwana wa Nimusi, anakonzera Yehoramu chiwembu. Yehoramu ankalondera Ramoti-giliyadi+ pamodzi ndi Aisiraeli onse, chifukwa cha Hazaeli+ mfumu ya Siriya.