-
2 Mafumu 9:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Ku Yezereeliko, mlonda amene anaima pansanja anaona gulu lankhondo la Yehu likubwera. Nthawi yomweyo mlondayo anati: “Ndikuona gulu la anthu likubwera.” Yehoramu anati: “Uza munthu wokwera hatchi kuti apite kukakumana nawo. Akawafunse kuti, ‘Kodi mukubwerera zamtendere?’”
-