-
2 Mafumu 9:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Ndiyeno mlonda uja ananena kuti: “Munthu tamutuma uja wakumana nawo, koma nayenso sakubwerera. Ndipo mmene anthuwo akuthamangira, akuthamanga ngati Yehu mdzukulu wa Nimusi, chifukwa iye amathamangitsa galeta ngati wamisala.”
-