-
2 Mafumu 9:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Yehoramu atamva zimenezi, anati: “Mangirirani mahatchi kugaleta!” Choncho anamangiriradi mahatchi kugaleta lake lankhondo. Ndiyeno Yehoramu mfumu ya Isiraeli ndi Ahaziya+ mfumu ya Yuda, ananyamuka aliyense pagaleta lake lankhondo, kupita kukakumana ndi Yehu ndipo anakumana naye pamunda wa Naboti+ wa ku Yezereeli.
-