2 Mafumu 9:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Yehoramu atangoona Yehu, anamʼfunsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji pali uhule wa Yezebeli+ mayi ako ndi zamatsenga zake zambirimbiri?”+
22 Yehoramu atangoona Yehu, anamʼfunsa kuti: “Kodi ukubwerera zamtendere Yehu?” Koma Yehu anayankha kuti: “Mtendere ungakhalepo bwanji pali uhule wa Yezebeli+ mayi ako ndi zamatsenga zake zambirimbiri?”+