25 Kenako Yehu anauza Bidikara msilikali wake womuthandiza, kuti: “Munyamule umuponye mʼmunda wa Naboti wa ku Yezereeli.+ Kumbukira kuti iwe ndi ine tinkabwera pambuyo pa Ahabu bambo ake, aliyense atakwera pagaleta lake la mahatchi awiri, pa nthawi imene Yehova anamutemberera kuti:+