2 Mafumu 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Yehova wanena kuti: “Ndithu magazi a Naboti+ ndi magazi a ana ake amene ndawaona dzulo, ndidzawabwezera+ pa iwe mʼmunda uwu,” watero Yehova.’ Choncho munyamule umuponye mʼmundamo mogwirizana ndi mawu a Yehova.”+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:26 Nsanja ya Olonda,2/1/2014, ptsa. 13-14
26 ‘Yehova wanena kuti: “Ndithu magazi a Naboti+ ndi magazi a ana ake amene ndawaona dzulo, ndidzawabwezera+ pa iwe mʼmunda uwu,” watero Yehova.’ Choncho munyamule umuponye mʼmundamo mogwirizana ndi mawu a Yehova.”+