-
2 Mafumu 9:27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
27 Ahaziya+ mfumu ya Yuda ataona zimenezi, anayamba kuthawa kudzera njira yakumunda.* (Kenako Yehu anayamba kumʼtsatira ndipo anati: “Ameneyonso mʼbayeni!” Choncho anamʼbayadi ali mʼgaleta lake pamene ankathawira ku Guru kufupi ndi ku Ibuleamu.+ Koma anapitirizabe kuthawa mpaka ku Megido kumene anakafera.
-