2 Mafumu 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Kenako atumiki ake anamunyamula mʼgaleta nʼkupita naye ku Yerusalemu ndipo anakamuika mʼmanda ake mu Mzinda wa Davide+ pamalo amene panagona makolo ake.
28 Kenako atumiki ake anamunyamula mʼgaleta nʼkupita naye ku Yerusalemu ndipo anakamuika mʼmanda ake mu Mzinda wa Davide+ pamalo amene panagona makolo ake.