2 Mafumu 9:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Yehu atafika ku Yezereeli,+ Yezebeli+ anamva zimenezo. Choncho Yezebeliyo anapaka zodzikongoletsera zakuda mʼzikope zake komanso anakonza tsitsi lake. Atatero anakaima pawindo nʼkumayangʼana kunja. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:30 Kuyankha Mafunso a M’Baibulo,
30 Yehu atafika ku Yezereeli,+ Yezebeli+ anamva zimenezo. Choncho Yezebeliyo anapaka zodzikongoletsera zakuda mʼzikope zake komanso anakonza tsitsi lake. Atatero anakaima pawindo nʼkumayangʼana kunja.