2 Mafumu 9:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Yehu anakweza maso kuyangʼana pawindopo nʼkufunsa kuti: “Ndani ali kumbali yanga? Ndani?”+ Nthawi yomweyo nduna ziwiri kapena zitatu za panyumba ya mfumu zinasuzumira pawindo kuyangʼana Yehu.
32 Yehu anakweza maso kuyangʼana pawindopo nʼkufunsa kuti: “Ndani ali kumbali yanga? Ndani?”+ Nthawi yomweyo nduna ziwiri kapena zitatu za panyumba ya mfumu zinasuzumira pawindo kuyangʼana Yehu.