-
2 Mafumu 9:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 Ndiyeno Yehu anati: “Mʼponyeni pansi Yezebeliyo!” Iwo anamʼponyadi pansi ndipo magazi ake ena anagwera pakhoma ndi pamahatchi. Kenako Yehu anamʼpondaponda ndi mahatchi ake.
-