2 Mafumu 9:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Anthuwo atabwerera kwa Yehu kukamuuza, iye anati: “Zimenezi zakwaniritsa mawu a Yehova+ amene ananena kudzera mwa mtumiki wake Eliya wa ku Tisibe, akuti: ‘Mʼmunda wa ku Yezereeli, agalu adzadya thupi la Yezebeli.+ 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:36 Yeremiya, tsa. 120
36 Anthuwo atabwerera kwa Yehu kukamuuza, iye anati: “Zimenezi zakwaniritsa mawu a Yehova+ amene ananena kudzera mwa mtumiki wake Eliya wa ku Tisibe, akuti: ‘Mʼmunda wa ku Yezereeli, agalu adzadya thupi la Yezebeli.+