2 Mafumu 10:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ku Samariya kunali ana aamuna a Ahabu+ okwana 70. Choncho Yehu analemba makalata nʼkuwatumiza ku Samariya kwa atsogoleri a ku Yezereeli, kwa akuluakulu+ ndiponso kwa anthu amene ankasamalira ana a Ahabu. Mʼmakalatamo analembamo kuti:
10 Ku Samariya kunali ana aamuna a Ahabu+ okwana 70. Choncho Yehu analemba makalata nʼkuwatumiza ku Samariya kwa atsogoleri a ku Yezereeli, kwa akuluakulu+ ndiponso kwa anthu amene ankasamalira ana a Ahabu. Mʼmakalatamo analembamo kuti: