-
2 Mafumu 10:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Choncho woyangʼanira nyumba ya mfumu, woyangʼanira mzinda, akuluakulu komanso amene ankasamalira ana a Ahabu, anatumiza uthenga kwa Yehu, wakuti: “Ife ndife atumiki anu ndipo tichita chilichonse chimene mungatiuze. Sitisankha munthu aliyense kuti akhale mfumu yathu. Inuyo chitani chilichonse chimene mukuona kuti nʼchabwino.”
-