-
2 Mafumu 10:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Kenako Yehu anawalemberanso kalata ina yonena kuti: “Ngati muli kumbali yanga ndipo muzimvera mawu anga, mudule mitu ya ana aamuna a mbuye wanu ndipo mawa nthawi ngati yomwe ino mubwere nayo ku Yezereeli kuno.”
Ana 70 a mfumuwo ankakhala ndi akuluakulu a mumzindawo omwe ankawasamalira.
-