2 Mafumu 10:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo atangolandira kalatayo, anatenga ana a mfumu 70 aja nʼkuwapha.+ Kenako anatenga mitu yawo nʼkuiika mʼmadengu ndipo anaitumiza kwa Yehu ku Yezereeli.
7 Anthuwo atangolandira kalatayo, anatenga ana a mfumu 70 aja nʼkuwapha.+ Kenako anatenga mitu yawo nʼkuiika mʼmadengu ndipo anaitumiza kwa Yehu ku Yezereeli.