2 Mafumu 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mʼmawa kutacha, Yehu anapita kukaima patsogolo pa anthu onse nʼkunena kuti: “Anthu inu ndinu osalakwa. Ine ndinachitira chiwembu mbuye wanga ndipo ndinamupha,+ koma ndani wapha anthu onsewa?
9 Mʼmawa kutacha, Yehu anapita kukaima patsogolo pa anthu onse nʼkunena kuti: “Anthu inu ndinu osalakwa. Ine ndinachitira chiwembu mbuye wanga ndipo ndinamupha,+ koma ndani wapha anthu onsewa?