-
2 Mafumu 10:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Kenako Yehu ananyamuka kupita ku Samariya. Ali pa ulendowo, anafika panyumba imene abusa ankameteramo ubweya wa nkhosa.
-