2 Mafumu 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kumeneko Yehu anakumana ndi abale ake a Ahaziya+ mfumu ya Yuda ndipo anawafunsa kuti, “Ndinu ndani?” Iwo anayankha kuti: “Ndife abale ake a Ahaziya ndipo tikupita kukaona ngati ana a mfumu ndi ana a mfumukazi ali bwino.”
13 Kumeneko Yehu anakumana ndi abale ake a Ahaziya+ mfumu ya Yuda ndipo anawafunsa kuti, “Ndinu ndani?” Iwo anayankha kuti: “Ndife abale ake a Ahaziya ndipo tikupita kukaona ngati ana a mfumu ndi ana a mfumukazi ali bwino.”