2 Mafumu 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi yomweyo Yehu anati: “Agwireni amoyo anthuwa!” Choncho anawagwiradi amoyo nʼkukawaphera pachitsime cha panyumba imene abusa ankameteramo ubweya wa nkhosa. Onse 42 anawapha ndipo palibe amene anamusiya ndi moyo.+
14 Nthawi yomweyo Yehu anati: “Agwireni amoyo anthuwa!” Choncho anawagwiradi amoyo nʼkukawaphera pachitsime cha panyumba imene abusa ankameteramo ubweya wa nkhosa. Onse 42 anawapha ndipo palibe amene anamusiya ndi moyo.+