2 Mafumu 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana* ndi Yehova.”+ Choncho Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo mʼgaleta lankhondo la Yehu. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda,1/1/1998, ptsa. 12-13
16 Kenako anamuuza kuti: “Tiye tipitire limodzi ukaone kuti sindilekerera zoti anthu azipikisana* ndi Yehova.”+ Choncho Yehonadabu anapita limodzi ndi anthuwo mʼgaleta lankhondo la Yehu.