2 Mafumu 10:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Kenako Yehu anafika ku Samariya ndipo anapha anthu onse a mʼbanja la Ahabu amene anatsala ku Samariya, mpaka onse anatha,+ mogwirizana ndi mawu a Yehova amene anauza Eliya.+
17 Kenako Yehu anafika ku Samariya ndipo anapha anthu onse a mʼbanja la Ahabu amene anatsala ku Samariya, mpaka onse anatha,+ mogwirizana ndi mawu a Yehova amene anauza Eliya.+