-
2 Mafumu 10:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ndiye itanani aneneri onse a Baala,+ anthu onse amene amamulambira ndiponso ansembe ake onse+ kuti abwere kwa ine. Pasapezeke aliyense wotsala chifukwa ndakonza nsembe yaikulu yoti ndipereke kwa Baala. Aliyense amene sabwera aphedwa.” Koma Yehu anawapusitsa nʼcholinga choti aphe anthu olambira Baala.
-