-
2 Mafumu 10:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Tsopano iye anauza munthu amene ankayangʼanira chipinda chosungira zovala kuti: “Bweretsa zovala zoti anthu onse omwe amalambira Baala avale.” Choncho iye anawabweretseradi zovalazo.
-