2 Mafumu 10:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Koma Yehu sanayesetse kutsatira Chilamulo cha Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+ Sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha Yerobowamu.+
31 Koma Yehu sanayesetse kutsatira Chilamulo cha Yehova Mulungu wa Isiraeli ndi mtima wake wonse.+ Sanasiye kuchita machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha Yerobowamu.+