2 Mafumu 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mʼmasiku amenewo, Yehova anayamba kuchepetsa dziko la Isiraeli pangʼono ndi pangʼono. Ndipo Hazaeli anapitiriza kuukira Aisiraeli mʼmadera awo onse.+
32 Mʼmasiku amenewo, Yehova anayamba kuchepetsa dziko la Isiraeli pangʼono ndi pangʼono. Ndipo Hazaeli anapitiriza kuukira Aisiraeli mʼmadera awo onse.+