2 Mafumu 10:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Kenako Yehu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anamuika mʼmanda ku Samariya. Ndiyeno Yehoahazi+ mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.
35 Kenako Yehu, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anamuika mʼmanda ku Samariya. Ndiyeno Yehoahazi+ mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.