2 Mafumu 11:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ataliya,+ mayi ake a Ahaziya ataona kuti mwana wawo wafa,+ anapha anthu onse amene anali oyenera kulowa ufumu.*+
11 Ataliya,+ mayi ake a Ahaziya ataona kuti mwana wawo wafa,+ anapha anthu onse amene anali oyenera kulowa ufumu.*+