-
2 Mafumu 11:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Koma Yehoseba mwana wamkazi wa Mfumu Yehoramu, mchemwali wake wa Ahaziya, anaba Yehoasi+ mwana wamwamuna wa Ahaziya, pagulu la ana aamuna a mfumu amene ankayenera kuphedwa. Anatenga Yehoasi ndi mayi amene ankamusamalira nʼkukawaika mʼchipinda chamkati chogona. Anakwanitsa kubisa mwanayo kuti Ataliya asamuone, moti sanaphedwe.
-