-
2 Mafumu 11:6Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
6 Gulu lina lidzakhale pageti lotchedwa Maziko ndipo gulu lachitatu lidzakhale pageti kumbuyo kwa asilikali olondera nyumba yachifumu. Muzidzasinthana kulondera nyumbayo.
-