-
2 Mafumu 11:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Wansembeyo anapatsa atsogoleri a magulu a asilikali 100 aja mikondo ndi zishango zozungulira zimene zinali za Mfumu Davide, zomwe zinali mʼnyumba ya Yehova.
-