-
2 Mafumu 11:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Choncho anthu onse amʼdzikolo anasangalala ndipo mumzindawo munali bata chifukwa Ataliya anali ataphedwa ndi lupanga panyumba ya mfumu.
-