2 Mafumu 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Koma sanachotse malo okwezeka+ ndipo anthu ankaperekabe nsembe zautsi komanso nsembe zina mʼmalo okwezekawo.
3 Koma sanachotse malo okwezeka+ ndipo anthu ankaperekabe nsembe zautsi komanso nsembe zina mʼmalo okwezekawo.