-
2 Mafumu 12:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Yehoasi anauza ansembe kuti: “Mutenge ndalama zonse zimene anthu akubweretsa kunyumba ya Yehova za zopereka zopatulika,+ zomwe ndi ndalama za msonkho zimene munthu aliyense akupereka,+ ndalama zoperekedwa ndi anthu amene analonjeza ndiponso ndalama zonse zimene munthu aliyense watsimikiza mumtima mwake kuti abweretse kunyumba ya Yehova.+
-