2 Mafumu 12:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iwo ankapereka ndalama zimene awerengazo kwa anthu amene ankayangʼanira ntchito yokonza nyumba ya Yehova. Anthuwo ankagwiritsa ntchito ndalamazo polipira akalipentala, anthu omwe ankagwira ntchito yomanga panyumba ya Yehovayo,+
11 Iwo ankapereka ndalama zimene awerengazo kwa anthu amene ankayangʼanira ntchito yokonza nyumba ya Yehova. Anthuwo ankagwiritsa ntchito ndalamazo polipira akalipentala, anthu omwe ankagwira ntchito yomanga panyumba ya Yehovayo,+