-
2 Mafumu 12:12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 amisiri omanga ndi miyala ndi anthu osema miyala. Ndalamazo anaguliranso matabwa ndi miyala yosema yokonzera nyumba ya Yehova ndiponso analipirira zonse zimene anagwiritsa ntchito pokonza nyumbayo.
-