2 Mafumu 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Anthu amene ankapatsidwa ndalama kuti azilipira anthu ogwira ntchito, sankafunsidwa mmene ayendetsera ndalamazo chifukwa anali okhulupirika.+
15 Anthu amene ankapatsidwa ndalama kuti azilipira anthu ogwira ntchito, sankafunsidwa mmene ayendetsera ndalamazo chifukwa anali okhulupirika.+