2 Mafumu 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehoahazi anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo sanasiye tchimo limene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Iye anapitiriza kuchita tchimolo.
2 Yehoahazi anapitiriza kuchita zoipa pamaso pa Yehova ndipo sanasiye tchimo limene Aisiraeli ankachita chifukwa cha Yerobowamu mwana wa Nebati.+ Iye anapitiriza kuchita tchimolo.