2 Mafumu 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho Yehova anakwiyira+ kwambiri Aisiraeli+ ndipo ankawapereka mʼmanja mwa Hazaeli+ mfumu ya Siriya ndi mʼmanja mwa Beni-hadadi+ mwana wa Hazaeli.
3 Choncho Yehova anakwiyira+ kwambiri Aisiraeli+ ndipo ankawapereka mʼmanja mwa Hazaeli+ mfumu ya Siriya ndi mʼmanja mwa Beni-hadadi+ mwana wa Hazaeli.