2 Mafumu 13:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 (Koma sanasiye machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha anthu amʼnyumba ya Yerobowamu.+ Iwo anapitiriza kuchita machimowo ndipo mzati wopatulika*+ unalipobe ku Samariya.)
6 (Koma sanasiye machimo amene Aisiraeli anachita chifukwa cha anthu amʼnyumba ya Yerobowamu.+ Iwo anapitiriza kuchita machimowo ndipo mzati wopatulika*+ unalipobe ku Samariya.)