2 Mafumu 13:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Yehoahazi anangotsala ndi asilikali 50 okwera pamahatchi, magaleta 10 ndi asilikali 10,000 oyenda pansi, chifukwa mfumu ya Siriya inawawononga+ ndi kuwapondaponda ngati fumbi la pa nthawi yopuntha mbewu.+
7 Yehoahazi anangotsala ndi asilikali 50 okwera pamahatchi, magaleta 10 ndi asilikali 10,000 oyenda pansi, chifukwa mfumu ya Siriya inawawononga+ ndi kuwapondaponda ngati fumbi la pa nthawi yopuntha mbewu.+