2 Mafumu 13:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Yehoahazi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anamuika mʼmanda ku Samariya.+ Ndiyeno Yehoasi mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.
9 Kenako Yehoahazi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo anamuika mʼmanda ku Samariya.+ Ndiyeno Yehoasi mwana wake anakhala mfumu mʼmalo mwake.