2 Mafumu 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako Yehoasi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo Yerobowamu*+ anakhala pampando wake wachifumu. Yehoasi anaikidwa ku Samariya mʼmanda a mafumu a Isiraeli.+
13 Kenako Yehoasi, mofanana ndi makolo ake, anamwalira ndipo Yerobowamu*+ anakhala pampando wake wachifumu. Yehoasi anaikidwa ku Samariya mʼmanda a mafumu a Isiraeli.+