2 Mafumu 13:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Elisa+ atayamba kudwala matenda amene pamapeto pake anafa nawo, Yehoasi mfumu ya Isiraeli anapita kukamuona ndipo anayamba kulira kuti: “Bambo anga ine! Bambo anga ine! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera pamahatchi ake!”+
14 Elisa+ atayamba kudwala matenda amene pamapeto pake anafa nawo, Yehoasi mfumu ya Isiraeli anapita kukamuona ndipo anayamba kulira kuti: “Bambo anga ine! Bambo anga ine! Galeta lankhondo la Isiraeli ndi okwera pamahatchi ake!”+