2 Mafumu 13:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Elisa anamwalira ndipo anamuika mʼmanda. Panali magulu a achifwamba a ku Mowabu+ amene ankabwera mʼdzikolo kumayambiriro kwa chaka chilichonse.
20 Kenako Elisa anamwalira ndipo anamuika mʼmanda. Panali magulu a achifwamba a ku Mowabu+ amene ankabwera mʼdzikolo kumayambiriro kwa chaka chilichonse.