2 Mafumu 13:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Tsiku lina anthu akuika maliro, anaona gulu la achifwamba. Nthawi yomweyo iwo anaponya mtembo wa munthuyo mʼmanda a Elisa nʼkuthawa. Mtembowo utakhudza mafupa a Elisa, munthuyo anauka+ ndipo anaimirira. 2 Mafumu Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:21 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2017, tsa. 5 Nsanja ya Olonda,8/1/2005, tsa. 1111/15/1991, tsa. 5
21 Tsiku lina anthu akuika maliro, anaona gulu la achifwamba. Nthawi yomweyo iwo anaponya mtembo wa munthuyo mʼmanda a Elisa nʼkuthawa. Mtembowo utakhudza mafupa a Elisa, munthuyo anauka+ ndipo anaimirira.
13:21 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2017, tsa. 5 Nsanja ya Olonda,8/1/2005, tsa. 1111/15/1991, tsa. 5