2 Mafumu 13:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Komabe Yehova anakomera mtima Aisiraeli nʼkuwachitira chifundo+ ndipo anasonyeza kuti ankawadera nkhawa chifukwa cha pangano limene anachita ndi Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+ Iye sanafune kuwawononga ndipo sanawachotse pamaso pake mpaka lero.
23 Komabe Yehova anakomera mtima Aisiraeli nʼkuwachitira chifundo+ ndipo anasonyeza kuti ankawadera nkhawa chifukwa cha pangano limene anachita ndi Abulahamu,+ Isaki+ ndi Yakobo.+ Iye sanafune kuwawononga ndipo sanawachotse pamaso pake mpaka lero.