2 Mafumu 14:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mʼchaka chachiwiri cha Yehoasi+ mwana wa Yehoahazi mfumu ya Isiraeli, Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, anakhala mfumu.
14 Mʼchaka chachiwiri cha Yehoasi+ mwana wa Yehoahazi mfumu ya Isiraeli, Amaziya mwana wa Yehoasi mfumu ya Yuda, anakhala mfumu.