2 Mafumu 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Amaziya anali ndi zaka 25 pamene anakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Yehoadini.+
2 Amaziya anali ndi zaka 25 pamene anakhala mfumu ndipo analamulira ku Yerusalemu zaka 29. Mayi ake anali a ku Yerusalemu ndipo dzina lawo linali Yehoadini.+